Psalms 107:26 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zombozo zidakwera mpaka m'mwamba nkutsikiranso kwakuya, ndipo anthuwo adataya mtima pa mavuto aowo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Akwera kuthambo, atsikira kozama; mtima wao usungunuka nacho choipacho.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Sitima za pamadzizo zinatukulidwa mmwamba ndi kutsikira pansi pakuya; pamene amawonongeka, kulimba mtima kwawo kunasungunuka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Akwera kuthambo, atsikira kozama; Mtima wao usungunuka naco coipaco.