Psalms 107:27 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adachita chizungulire namadzandira ngati anthu oledzera, kenaka nkuthedwa nzeru.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Adzandira napambanitsa miyendo ngati munthu woledzera, nathedwa nzeru konse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anachita chizungulire ndi kudzandira ngati anthu oledzera; anali pa mapeto a moyo wawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Adzandira napambanitsa miyendo ngati munthu woledzeta, Nathedwa nzeru konse.