Psalms 107:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Waŵasonkhanitsa kuchokera ku maiko onse, kuchokera kuvuma ndi kuzambwe, kumpoto ndi kumwera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nawasokolotsa kumaiko, kuchokera kum'mawa ndi kumadzulo, kumpoto ndi kunyanja.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
iwo amene anawasonkhanitsa kuchokera ku mayiko, kuchokera kumadzulo ndi kummawa, kuchokera kumpoto ndi kummwera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nawasokolotsa kumaiko, Kucokera kum'mawa ndi kumadzulo, Kumpoto ndi kunyanja.