Psalms 107:34 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
dziko lachonde adalisandutsa nthaka yamchere, chifukwa cha kuipa kwa anthu okhala m'menemo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Dziko la zipatso, likhale lakhulo, chifukwa cha choipa cha iwo okhalamo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndiponso nthaka yachonde kukhala nthaka yamchere, chifukwa cha kuyipa kwa amene amakhala kumeneko.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Dziko lazipatso, likhale lakhulo, Cifukwa ca coipa ca iwo okhalamo.