Psalms 107:35 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Komanso adasandutsa chipululu kuti chikhale ndi maiŵe a madzi, nthaka youma kuti ikhale akasupe a madzi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Asanduliza chipululu chikhale thawale, ndi dziko louma likhale akasupe a madzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anasandutsa chipululu kukhala mayiwe a madzi ndi nthaka yowuma kukhala akasupe a madzi oyenda;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Asanduliza cipululu cikhale tha wale, Ndi dziko louma likhale akasupe a madzi.