Psalms 107:36 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo kumeneko Chauta adakhazikako anthu anjala, tsono anthuwo adamanga mzinda woti azikhalamo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi apo akhalitsa anjala, kuti amangeko mudzi wokhalamo anthu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kumeneko Iye anabweretsa anthu anjala kuti azikhalako, ndipo iwo anamanga mzinda woti akhazikikeko.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi apo akhalitsa anjala, Kuti amangeko mudzi wokhalamo anthu;