Psalms 107:38 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chifukwa cha madalitso a Chauta, anthuwo adachuluka kwambiri, Chauta sadalole kuti zoŵeta za anthuwo zichepe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo awadalitsa, kotero kuti achuluka kwambiri; osachepsanso zoweta zao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova anawadalitsa, ndipo chiwerengero chawo chinachuluka kwambiri, ndipo Iye sanalole kuti ziweto zawo zithe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo awadalitsa, kotero kuti, acuruka kwambiri; Osacepsanso zoweta zao.