Psalms 107:39 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene anthu ake chiŵerengero chao chidachepa, ndipo pamene adatsitsidwa chifukwa cha mazunzo, mavuto ndi chisoni,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma achepanso, nawerama, chifukwa cha chisautso, choipa ndi chisoni.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka chiwerengero chawo chinachepa ndipo iwo anatsitsidwa chifukwa cha mazunzo, mavuto ndi chisoni;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma acepanso, nawerama, Cifukwa ca cisautso, coipa ndi cisoni.