Psalms 107:41 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma anthu osoŵa adaŵatulutsa m'mavuto ao, adachulukitsa mabanja ao ngati magulu a nkhosa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma aika waumphawi pamsanje posazunzika, nampatsa mabanja ngati gulu la nkhosa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Iyeyo anakweza anthu osowa kuchoka ku masautso awo ngati magulu a nkhosa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma aika waumphawi pamsanje posazunzika, Nampatsa mabanja ngati gulu la nkhosa.