Psalms 107:42 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu olungama mtima amaona zimenezo, nkumasangalala, koma oipa onse amaŵakhalitsa chete.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Oongoka mtima adzachiona nadzasekera; koma chosalungama chonse chitseka pakamwa pake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu olungama mtima amaona ndi kusangalala, koma anthu onse oyipa amatseka pakamwa pawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Oongoka mtima adzaciona nadzasekera; Koma cosalungama conse citseka pakamwa pace.