Psalms 107:43 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Munthu aliyense wanzeru asamale zimenezi, anthu alingalire za chikondi chosasinthika cha Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wokhala nazo nzeru asamalire izi, ndipo azindikire zachifundo za Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Aliyense wanzeru asamalitse zinthu zimenezi ndi kuganizira za chikondi chachikulu cha Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wokhala nazo nzeru asamalire izi, Ndipo azindikire zacifundo za Yehova,