Psalms 107:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta amapha ludzu la munthu womva ludzu, amamudyetsa zinthu zabwino munthu womva njala.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti akhutitsa mtima wolakalaka, nadzaza mtima wanjala ndi zabwino.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
pakuti Iye wapha ludzu la munthu womva ludzu ndipo wakhutitsa wanjala ndi zinthu zabwino.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti akhutitsa mtima wolakalaka, Nadzaza mtima wanjala ndi zabwino.