Psalms 108:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu Mulungu, mtima wanga wakonzeka, ndithu, mtima wanga wakonzekadi! Ndidzaimba nyimbo, nyimbo yake yotamanda. Lumpha, iwe mtima wanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nyimbo. Salimo la Davide. Wakhazikika mtima wanga, Mulungu; ndidzaimba, inde ndidzaimba zolemekeza, ndiko ulemerero wanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nyimbo. Salimo la Davide. Mtima wanga ndi wokhazikika, Inu Mulungu; ndidzayimba nyimbo, inde ndidzayimba nyimbo zotamanda ndi moyo wanga wonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wakhazikika mtima wanga, Mulungu; Ndidzayimba, inde ndidzayimba zolemekeza, ndiko ulemerero wanga.