Psalms 108:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu zeze ndi pangwe, tiyeni lirani. Ndidzadzutsa dzuŵa ndi nyimbo zanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Galamukani, chisakasa ndi zeze; ndidzauka ndekha mamawa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Dzukani, zeze ndi pangwe! Ine ndidzadzutsa mʼbandakucha.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Galamukani, cisakasa ndi zeze; Ndidzauka ndekha mamawa.