Psalms 108:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidzakuthokozani, Inu Chauta, pakati pa mitundu ya anthu. Ndidzaimba nyimbo zokutamandani pakati pa anthu a m'maiko onse,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndidzakuyamikani mwa mitundu ya anthu, Yehova: ndipo ndidzaimba zakukulemekezani mwa anthu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndidzakutamandani Yehova, pakati pa anthu a mitundu ina; ndidzayimba za Inu pakati pa anthu a mitundu ina.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndidzakuyamikani mwa mitundu ya anthu, Yehova: Ndipo ndidzayimba zakukulemekezani mwa anthu.