Psalms 108:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
pakuti chikondi chanu chosasinthika nchachikulu, chofika mpaka pamwamba pa mlengalenga, kukhulupirika kwanu kumafika mpaka ku mitambo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti chifundo chanu nchachikulu kupitirira kumwamba, ndi choonadi chanu kufikira mitambo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti chikondi chanu nʼchachikulu, kutalika kwake kuposa kumwamba; kukhulupirika kwanu kumafika mlengalenga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti cifundo canu ncacikuru kupitirira kumwamba, Ndi coonadi canu kufikira mitambo.