Psalms 109:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pasapezeke ndi mmodzi yemwe womukomera mtima, kapena wina woŵachitira chifundo ana ake amasiye aja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pasakhale munthu wakumchitira chifundo; kapena kuchitira chokoma ana ake amasiye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pasapezeke ndi mmodzi yemwe womukomera mtima kapena kumvera chisoni ana ake amasiye.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pasakhale munthu wakumdtira cifundo; Kapena kucitira cokoma ana ace amasiye.