Psalms 109:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
pakuti anthu oipa ndi onama amakamba zondiwukira, amalankhula zondinamizira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pakuti pakamwa pa woipa ndi pakamwa pa chinyengo pananditsegukira; anandilankhulira ndi m'kamwa mwa bodza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
pakuti anthu oyipa ndi achinyengo atsekula pakamwa pawo kutsutsana nane; iwo ayankhula motsutsana nane ndi malilime abodza.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti pakamwa pa woipa ndi pakamwa pa cinyengo pananditsegukira; Anandilankhulira ndi m'kamwa mwa bodza.