Psalms 109:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zimenezi zikhale chilango chochokera kwa Chauta kugwera ondineneza. Ziŵagwere amene amalankhula zoipira moyo wanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ichi chikhale mphotho ya otsutsana nane yowapatsa Yehova, ndi ya iwo akunenera choipa moyo wanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Awa akhale malipiro ochokera kwa Yehova pa onditsutsa anga, kwa iwo amene amayankhula zoyipa za ine.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ici cikhale mphotho ya otsutsana nane yowapatsa Yehova, Ndi ya iwo akunenera coipa moyo wanga.