Psalms 109:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Inu Mulungu, Ambuye anga, munditchinjirize malinga ndi ulemerero wa dzina lanu, mundipulumutse chifukwa chikondi chanu chosasinthika ndi chabwino.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Inu, Yehova Ambuye, muchite nane chifukwa cha dzina lanu; ndilanditseni popeza chifundo chanu ndi chabwino.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Inu Ambuye Wamphamvuzonse, muchite nane molingana ndi dzina lanu, chifukwa cha ubwino wa chikondi chanu, pulumutseni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Inu, Yehova Ambuye, mucite nane cifukwa ca dzina lanu; Ndilanditseni popeza cifundo canu ndi cabwino.