Psalms 109:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakuti ine ndine wosauka ndi wosoŵa, ndipo mtima wanga ukuŵaŵa kwambiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti ine ndine wozunzika ndi waumphawi, ndi mtima wanga walaswa m'kati mwanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti ndine wosauka ndi wosowa, ndipo mtima wanga ukuwawa mʼkati mwanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti ine ndine wozunzika ndi waumphawi, Ndi mtima wanga walaswa m'kati mwanga.