Psalms 109:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndazimirira ngati mthunzi wamadzulo, ndapirikitsidwa ngati dzombe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndamuka ngati mthunzi womka m'tali; ndiingidwa kwina ndi kwina ngati dzombe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndikuzimirira ngati mthunzi wa kumadzulo, ndapirikitsidwa ngati dzombe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndamuka ngati mthunzi womka m'tali Ndiingidwa kwina ndi kwina ngati dzombe.