Psalms 109:24 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Maondo anga afooka chifukwa chosala zakudya, thupi langa laonda ndi mutu womwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mabondo anga agwedezeka chifukwa cha kusala; ndi mnofu wanga waonda posowa mafuta.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mawondo anga afowoka chifukwa cha kusala zakudya, thupi langa lawonda ndi mutu wanga womwe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mabondo anga agwedezeka cifukwa ca kusala; Ndi mnofu wanga waonda posowa mafuta.