Psalms 109:25 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ondineneza amandinyodola, akandiwona amapukusa mitu yao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndiwakhaliranso chotonza; pakundiona apukusa mutu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndine chinthu chotonzedwa kwa otsutsana nane; akandiona, amapukusa mitu yawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndiwakhaliranso cotonza; Pakundiona apukusa mutu.