Psalms 109:26 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Thandizeni Chauta, Mulungu wanga. Pulumutseni chifukwa cha chikondi chanu chosasinthika.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndithandizeni Yehova, Mulungu wanga: Ndipulumutseni monga mwa chifundo chanu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Thandizeni Inu Yehova Mulungu wanga; pulumutseni molingana ndi chikondi chanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndithandizeni Yehova, Mulungu wanga: Ndipulumutseni monga mwa cifundo canu;