Psalms 109:27 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adani adziŵe kuti limeneli ndi dzanja lanu londipulumutsa, Inu Chauta, ndinu amene mwachita zimenezi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuti adziwe kuti ichi ndi dzanja lanu; kuti Inu Yehova munachichita.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Adaniwo adziwe kuti limeneli ndi dzanja lanu, kuti Inu Yehova mwachita zimenezi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kuti adziwe kuti ici ndi dzanja lanu; Kuti Inu Yehova munacicita.