Psalms 109:28 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwo atemberere, koma Inu mundidalitse. Ondiputa muŵachititse manyazi, koma ine mtumiki wanu ndisangalale.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Atemberere iwowa, koma mudalitse ndinu; pakuuka iwowa adzachita manyazi, koma mtumiki wanu adzakondwera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Angathe kutemberera, koma Inu mudzadalitsa; pamene iwo andiputa adzachititsidwa manyazi, koma mtumiki wanu adzasangalala.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Atemberere iwowa, koma mudalitse ndinu; Pakuuka iwowa adzacita manyazi, koma mtumiki wanu adzakondwera.