Psalms 109:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ponseponse amandilankhula mau achidani, amandinena popanda chifukwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anandizinga ndi mau a udani, nalimbana nane kopanda chifukwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Andizungulira ndi mawu audani, amandinena popanda chifukwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anandizinga ndi mau a udani, Nalimbana nane kopanda cifukwa.