Psalms 109:30 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidzathokoza Chauta kwambiri polankhula. Ndidzamtamanda pakati pa gulu la anthu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndidzayamika Yehova kwakukulu pakamwa panga; ndi pakati pa anthu aunyinji ndidzamlemekeza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndi pakamwa panga ndidzathokoza Yehova kwambiri; ndidzamutamanda mʼgulu lalikulu la anthu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndidzayamika Yehova kwakukuru pakamwa panga; Ndi pakati pa anthu aunyinji ndidzamlemekeza.