Psalms 109:31 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paja Chauta amaimirira pafupi ndi munthu wosoŵa, amafuna kumpulumutsa kwa anthu ogamula kuti iyeyo aphedwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Popeza adzaima pa dzanja lamanja la waumphawi, kumpulumutsa kwa iwo akuweruza koipa moyo wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Popeza Iye amayima ku dzanja lamanja la munthu wosowayo, kupulumutsa moyo wake kwa iwo amene agamula molakwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Popeza adzaima pa dzanja lamanja la waumphawi Kumpulumutsa kwa iwo akuweruza koipa moyo wace.