Psalms 109:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero amandibwezera zoipa m'malo mwa zabwino, amandiwonetsa chidani m'malo mwa chikondi changa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anandisenza choipa m'malo mwa chokoma, ndi udani m'malo mwa chikondi changa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo amandibwezera zoyipa mʼmalo mwa zabwino, ndi udani mʼmalo mwa chikondi changa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anandisenza coipa m'malo mwa cokoma, Ndi udani m'malo mwa cikondi canga.