Psalms 109:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Sankhulani munthu woipa kuti aweruze mlandu wa wondiwukirayo, iye aimbidwe mlandu ndi munthu woneneza anzake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Muike munthu woipa akhale mkulu wake; ndi mdani aime pa dzanja lamanja lake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Sankhani munthu woyipa kuti amutsutse iye; lolani wotsutsa ayime ku dzanja lake lamanja.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Muike munthu woipa akhale mkuru wace; Ndi mdani aime pa dzanja lamanja lace.