Psalms 109:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pomuweruza apezeke kuti ali ndi mlandu, mapemphero ake akhale ngati kupalamula.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ponenedwa mlandu wake atuluke wotsutsika; ndi pemphero lake likhale ngati kuchimwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene aweruzidwa, apezeke kuti ndi wolakwa, ndipo mapemphero ake amutsutse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ponenedwa mlandu wace aturuke wotsutsika; Ndi pemphero lace likhale ngati kucimwa.