Psalms 11:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndimathaŵira kwa Chauta. Nanga mungathe bwanji kundiwuza kuti, “Thaŵira ku mapiri ngati mbalame.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kwa Mkulu wa Nyimbo; Salimo la Davide. Ndakhulupirira Yehova, mutani nkunena kwa moyo wanga, Thawirani kuphiri lanu ngati mbalame?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kwa mtsogoleri wa mayimbidwe. Salimo la Davide. Mwa Yehova ine ndimathawiramo. Nanga mungathe bwanji kunena kwa ine kuti, “Thawira ku phiri lako ngati mbalame.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndakhulupirira Yehova: Mutani nkunena kwa moyo wanga, Thawirani ku phiri lanu ngati mbalame?