Psalms 11:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Taonani, anthu oipa akunga uta ndipo akwinja muvi pa nsinga, kuti alase anthu a mtima wolungama.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti, onani, oipa akoka uta, apiringidza muvi wao pansinga, kuwaponyera mumdima oongoka mtima.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti taona oyipa akunga mauta awo; ayika bwino mivi yawo pa zingwe za uta, pobisala pawo kuti alase olungama mtima.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti, onani, oipa akoka uta, Apiringidza mubvi wao pansinga, Kuwaponyera mumdima oongoka mtima.