Psalms 11:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Chauta ali m'Nyumba yake yoyera, Chauta mpando wake waufumu uli kumwamba. Maso ake amapenya anthu onse ndi kuŵayesa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova ali m'Kachisi wake woyera, Yehova, mpando wachifumu wake uli m'Mwamba; apenyerera ndi maso ake, ayesa ana a anthu ndi zikope zake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova ali mʼNyumba yake yoyera; Yehova ali pa mpando wake waufumu kumwamba. Iye amayangʼanitsitsa ana a anthu; maso ake amawayesa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova ali m'Kacisi wace woyera, Yehova, mpando wacifumu wace uli m'Mwamba; Apenyerera ndi maso ace, ayesa ana a anthu ndi zikope zace.