Psalms 11:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta amayesa anthu olungama namakondwera nawo, mtima wake umadana ndi anthu oipa okonda zachiwawa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova ayesa wolungama mtima, koma moyo wake umuda woipa ndi iye wakukonda chiwawa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova amayesa olungama, koma moyo wake umadana ndi oyipa, amene amakonda zachiwawa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova ayesa wolungama mtima: Koma moyo wace umuda woipa ndi iye wakukonda ciwawa.