Psalms 11:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iye adzaŵagwetsera makala ndi miyala yamoto ngati mvula, adzaŵalanga ndi mphepo yotentha monga kuŵayenera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Adzagwetsa pwatapwata misampha pa oipa; moto ndi miyala ya sulufure, ndi mphepo yoopsa zidzawagawikira m'chikho chao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye adzakhuthulira pa oyipa makala amoto ndi sulufule woyaka; mphepo yotentha idzakhala yowayenera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Adzagwetsa pwata pwata misampha pa oipa; Moto ndi miyala yasuifure, ndi mphepo yoopsa zidzawagawikira m'cikho cao.