Psalms 11:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paja Chauta ndi wolungama, amakonda ntchito zolungama, ndipo anthu olungama adzaona nkhope yake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti Yehova ndiye wolungama; akonda zolungama; woongoka mtima adzapenya nkhope yake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti Yehova ndi wolungama, Iye amakonda chilungamo; ndipo anthu olungama adzaona nkhope yake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti Yehova ndiye wolungama; akonda zolungama: Woongoka mtima adzapenya nkhope yace.