Psalms 110:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu ako adzadzipereka mwaufulu, pa tsiku limene udzaonetse mphamvu zako pa phiri loyera. Anyamata ako adzabwera kwa iwe mu unyinji wao, monga m'mene mame amabwerera m'mamaŵa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anthu anu adzadzipereka eni ake tsiku la chamuna chanu: M'moyera mokometsetsa, mobadwira matanda kucha, muli nao mame a ubwana wanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ankhondo ako adzakhala odzipereka pa tsiku lako la nkhondo. Atavala chiyero chaulemerero, kuchokera mʼmimba ya mʼbandakucha, udzalandira mame a unyamata wako.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anthu anu adzadzipereka eni ace tsiku la camuna canu: M'moyera mokometsetsa, mobadwira tnatanda kuca, Muli nae mame a ubwana wanu.