Psalms 110:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta walumbira ndipo sadzasintha maganizo ake akuti, “Ndiwe wansembe mpaka muyaya, unsembe wake wonga uja wa Melkizedeki.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova walumbira, ndipo sadzasintha, Inu ndinu wansembe kosatha monga mwa chilongosoko cha Melkizedeki.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova walumbira ndipo sadzasintha maganizo ake: “Ndiwe wansembe mpaka muyaya monga mwa unsembe wa Melikizedeki.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova walamulira, ndipo sadzasintha, Inu ndinu wansembe kosatha Monga mwa cilongosoko ca Melikizedeke.