Psalms 110:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ambuye ali pambali pako. Adzaphwanya mafumu pa tsiku la mkwiyo wao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova pa dzanja lamanja lako adzaphwanya mafumu tsiku la mkwiyo wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ambuye ali kudzanja lako lamanja; Iye adzaponda mafumu pa tsiku la ukali wake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova pa dzanja lamanja lako Adzaphwanya mafumu tsiku la mkwiyo wace.