Psalms 110:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adzalanga mitundu ya anthu akunja, adzadzaza dziko lapansi ndi mitembo. Adzagonjetsa olamulira a pa dziko lonse lapansi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Adzaweruza mwa amitundu, adzadzaza dziko ndi mitembo; adzaphwanya mitu m'maiko ambiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Adzaweruza anthu a mitundu ina, adzadzaza dziko lapansi ndi mitembo ndipo adzaphwanya olamulira a pa dziko lonse lapansi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Adzaweruza mwa amitundu, Adzadzaza dziko ndi mitembo; Adzaphwanya mitu m'maiko ambiri.