Psalms 110:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adzamwa mu mtsinje wam'njira, ndipo adzaŵeramutsa mutu monyadira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Adzamwa kumtsinje wa panjira; chifukwa chake adzaweramutsa mutu wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye adzamwa mu mtsinje wa mʼmbali mwa njira; choncho adzaweramutsa mutu wake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Adzamwa ku mtsinje wa panjira; Cifukwa cace adzaweramutsa mutu wace.