Psalms 111:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tamandani Chauta. Ndidzathokoza Chauta ndi mtima wanga wonse pa msonkhano wa anthu olungama mtima.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Aleluya. Ndidzayamika Yehova ndi mtima wonse, mu upo wa oongoka mtima, ndi mumsonkhano.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tamandani Yehova. Ndidzathokoza Yehova ndi mtima wanga wonse mʼbwalo la anthu olungama mtima ndi pa msonkhano.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Haleluya. Ndidzayamika Yehova ndi mtima wonse, Mu upo wa oongoka mtima, ndi mumsonkhano.