Psalms 111:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amatikumbutsa ntchito zake zodabwitsa, Chauta ndi wokoma ndi wachifundo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anachita chokumbukitsa zodabwitsa zake; Yehova ndiye wachisomo ndi nsoni zokoma.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye wachititsa kuti zodabwitsa zake zikumbukirike; Yehova ndi wokoma mtima ndi wachifundo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anacita cokumbukitsa zodabwiza zace; Yehova ndiye wa cisomo ndi nsoni zokoma.