Psalms 111:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amapatsa chakudya anthu omuwopa, amakumbukira chipangano chake nthaŵi zonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anapatsa akumuopa Iye chakudya; adzakumbukira chipangano chake kosatha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Amapereka chakudya kwa amene amamuopa Iye; amakumbukira pangano lake kwamuyaya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anapatsa akumuopa Iye cakudya; Adzakumbukila cipangano cace kosatha.