Psalms 111:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndi okhazikika mpaka muyaya, paja adaŵapereka ndi mtima wokhulupirika ndi wolungama.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Achirikizika kunthawi za nthawi, achitika m'choonadi ndi chilunjiko.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Malamulo ndi okhazikika ku nthawi za nthawi, ochitidwa mokhulupirika ndi molungama.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Acirikizika ku nthawi za nthawi, Acitika m'coonadi ndi cilunjiko,