Psalms 111:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adapulumutsa anthu ake. Adakhazikitsa chipangano chake kuti chikhale chamuyaya. Dzina lake ndi loyera ndi loopsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anatumizira anthu ake chipulumutso; analamulira chipangano chake kosatha; dzina lake ndilo loyera ndi loopedwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iyeyo amawombola anthu ake; anakhazikitsa pangano lake kwamuyaya dzina lake ndi loyera ndi loopsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anatumizira anthu ace cipulumutso; Analamulira cipangano cace kosatha; Dzina lace ndilo loyera ndi loopedwa.