Psalms 112:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tamandani Chauta! Ngwodala munthu woopa Chauta, wokonda kusunga malamulo ake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Aleluya. Wodala munthu wakuopa Yehova, wakukondwera kwambiri ndi malamulo ake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tamandani Yehova. Wodala munthu amene amaopa Yehova, amene amakondwera kwambiri ndi malamulo ake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Haleluya. Wodala munthu wakuopa Yehova, Wakukondwera kwambiri ndi malamulo ace,